Ekisodo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Aroni atangomaliza kulankhula ndi gulu lonse la Aisiraeli, iwo anatembenuka nʼkuyangʼana kuchipululu. Ndipo kenako ulemerero wa Yehova unaonekera mumtambo.+
10 Ndiyeno Aroni atangomaliza kulankhula ndi gulu lonse la Aisiraeli, iwo anatembenuka nʼkuyangʼana kuchipululu. Ndipo kenako ulemerero wa Yehova unaonekera mumtambo.+