Ekisodo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho madzulo amenewo kunabwera zinziri zimene zinakuta msasa wonse,+ ndipo mʼmawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:13 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, tsa. 14
13 Choncho madzulo amenewo kunabwera zinziri zimene zinakuta msasa wonse,+ ndipo mʼmawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo.