Ekisodo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho zinachitikadi kuti madzulo kunabwera zinziri+ zimene zinakuta msasa wonse, ndipo m’mawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:13 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, tsa. 14
13 Choncho zinachitikadi kuti madzulo kunabwera zinziri+ zimene zinakuta msasa wonse, ndipo m’mawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo.+