-
Numeri 11:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Kenako Yehova anautsa mphepo+ yamkokomo kuchokera kunyanja. Mphepoyo inabweretsa zinziri,+ ndipo inazimwaza kuyambira pamsasapo mpaka pamtunda woyenda tsiku limodzi kulowera mbali ina, ndiponso mtunda woyenda tsiku limodzi kulowera mbali inayo. Inazimwaza kuzungulira msasawo, moti zinali kuuluka m’munsi kwambiri pafupifupi mikono* iwiri kuchokera pansi.
-