Ekisodo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho zinachitikadi kuti madzulo kunabwera zinziri+ zimene zinakuta msasa wonse, ndipo m’mawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo.+ Salimo 78:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anagwetsa chakudya pa iwo ngati fumbi.+Anawagwetsera zolengedwa zamapiko zouluka, zochuluka ngati mchenga wakunyanja.+ Salimo 105:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anapempha nyama ndipo anawapatsa zinziri,+Anawadyetsa chakudya chochokera kumwamba.+
13 Choncho zinachitikadi kuti madzulo kunabwera zinziri+ zimene zinakuta msasa wonse, ndipo m’mawa kunachita mame kuzungulira msasa wonsewo.+
27 Iye anagwetsa chakudya pa iwo ngati fumbi.+Anawagwetsera zolengedwa zamapiko zouluka, zochuluka ngati mchenga wakunyanja.+