Salimo 78:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anachititsa mphepo ya kum’mawa kuwomba m’mlengalenga,+Ndipo mwa mphamvu zake anachititsa mphepo ya kum’mwera kuwomba.+ Salimo 135:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+Iye anapanganso zipata zotulukirapo mvula.+Amachititsa mphepo kutuluka m’nkhokwe zake.+
26 Anachititsa mphepo ya kum’mawa kuwomba m’mlengalenga,+Ndipo mwa mphamvu zake anachititsa mphepo ya kum’mwera kuwomba.+
7 Amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+Iye anapanganso zipata zotulukirapo mvula.+Amachititsa mphepo kutuluka m’nkhokwe zake.+