-
Ekisodo 16:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mʼmawa uliwonse iwo ankatola chakudyacho, aliyense mogwirizana ndi mmene amadyera. Dzuwa likatentha, chakudyacho chinkasungunuka.
-