Ekisodo 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo m’mawa uliwonse+ anali kukatola chakudyacho, aliyense malinga ndi mmene amadyera. Dzuwa likatentha, chinali kusungunuka.
21 Ndipo m’mawa uliwonse+ anali kukatola chakudyacho, aliyense malinga ndi mmene amadyera. Dzuwa likatentha, chinali kusungunuka.