Ekisodo 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Mose anati: “Yehova walamula kuti, ‘Dzazani muyezo umodzi wa omeri ndi mana kuti asungidwe mʼmibadwo yanu yonse,+ nʼcholinga choti iwo adzaone chakudya chimene ndinakupatsani mʼchipululu nditakutulutsani mʼdziko la Iguputo.’”
32 Kenako Mose anati: “Yehova walamula kuti, ‘Dzazani muyezo umodzi wa omeri ndi mana kuti asungidwe mʼmibadwo yanu yonse,+ nʼcholinga choti iwo adzaone chakudya chimene ndinakupatsani mʼchipululu nditakutulutsani mʼdziko la Iguputo.’”