Ekisodo 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamenepo Mose anati: “Yehova walamula kuti, ‘Dzazani muyezo umodzi wa omeri ndi mana kuti asungidwe m’mibadwo yanu yonse,+ n’cholinga choti adzaone mkate umene ndinakudyetsani m’chipululu pamene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.’”+
32 Pamenepo Mose anati: “Yehova walamula kuti, ‘Dzazani muyezo umodzi wa omeri ndi mana kuti asungidwe m’mibadwo yanu yonse,+ n’cholinga choti adzaone mkate umene ndinakudyetsani m’chipululu pamene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.’”+