Salimo 105:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+ Salimo 111:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye wakonza zoti ntchito zake zodabwitsa zizikumbukiridwa.+ ח [Chehth]Yehova ndi wachisomo ndiponso wachifundo.+
5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+ Salimo 111:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye wakonza zoti ntchito zake zodabwitsa zizikumbukiridwa.+ ח [Chehth]Yehova ndi wachisomo ndiponso wachifundo.+
4 Iye wakonza zoti ntchito zake zodabwitsa zizikumbukiridwa.+ ח [Chehth]Yehova ndi wachisomo ndiponso wachifundo.+