-
Ekisodo 18:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Tsiku lotsatira, Mose anakhala pansi monga mwa masiku onse kuti atumikire anthu monga woweruza, ndipo anthu ankaima pamaso pa Mose kuyambira mʼmawa mpaka madzulo.
-