Ekisodo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa tsiku lotsatira, Mose anakhala pansi monga mwa masiku onse kuti atumikire anthu monga woweruza,+ ndipo anthu anali kubwera ndi kuimirira pamaso pa Mose kuyambira m’mawa mpaka madzulo. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:13 Nsanja ya Olonda,2/1/2013, tsa. 6
13 Pa tsiku lotsatira, Mose anakhala pansi monga mwa masiku onse kuti atumikire anthu monga woweruza,+ ndipo anthu anali kubwera ndi kuimirira pamaso pa Mose kuyambira m’mawa mpaka madzulo.