Ekisodo 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu wamenya kapolo wake wamwamuna kapena kapolo wake wamkazi padiso nʼkumuvulaza kwambiri, azimasula kapoloyo ndipo azimulola kuchoka ngati malipiro a diso lake.+
26 Ngati munthu wamenya kapolo wake wamwamuna kapena kapolo wake wamkazi padiso nʼkumuvulaza kwambiri, azimasula kapoloyo ndipo azimulola kuchoka ngati malipiro a diso lake.+