Ekisodo 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Munthu akamenya kapolo wake wamwamuna kapena kapolo wake wamkazi padiso n’kumuvulaza kwambiri, azimasula kapoloyo ndi kumulola kuchoka monga malipiro a diso lake.+
26 “Munthu akamenya kapolo wake wamwamuna kapena kapolo wake wamkazi padiso n’kumuvulaza kwambiri, azimasula kapoloyo ndi kumulola kuchoka monga malipiro a diso lake.+