Ekisodo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwa zaka 6, muzidzala mbewu mʼminda yanu nʼkukolola mbewuzo.+