Ekisodo 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mʼdziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku a moyo wanu.*
26 Mʼdziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku a moyo wanu.*