Ekisodo 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mupange likasa* la mtengo wa mthethe, masentimita 110* mulitali, masentimita 70 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi kupita mʼmwamba.+
10 Mupange likasa* la mtengo wa mthethe, masentimita 110* mulitali, masentimita 70 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi kupita mʼmwamba.+