Ekisodo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mupangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo muwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+
18 Mupangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo muwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+