Ekisodo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Akerubiwo atambasule mapiko awo nʼkuwakweza mʼmwamba ndipo aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo.+ Iwo akhale moyangʼanizana, koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro.
20 Akerubiwo atambasule mapiko awo nʼkuwakweza mʼmwamba ndipo aphimbe chivundikirocho ndi mapiko awo.+ Iwo akhale moyangʼanizana, koma nkhope zawo ziweramire pachivundikiro.