-
Ekisodo 26:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Uike zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe pansalu imodzi, ndipo uikenso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe mʼmphepete mwa nsalu inayo kuti zikhale moyangʼanizana pamalo olumikizirana.
-