Ekisodo 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uike zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe pansalu imodzi, ndipo uikenso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe kumapeto kwa nsalu imene ili polumikizirana nsalu ziwirizo. Zingwezo zikhale moyang’anizana.+
5 Uike zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe pansalu imodzi, ndipo uikenso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe kumapeto kwa nsalu imene ili polumikizirana nsalu ziwirizo. Zingwezo zikhale moyang’anizana.+