Ekisodo 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Upange mafelemu 6 nʼkuwaika kumbuyo kwa chihemacho, mbali yakumadzulo.+