-
Ekisodo 26:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Mafelemu amenewa akhale ndi matabwa awiri ophatikiza kuyambira pansi mpaka pamwamba. Matabwawo alumikizane pamphete yoyamba. Mafelemu awiriwo apangidwe mofanana ndipo akhale ochirikiza mʼmakona.
-