-
Ekisodo 26:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Lililonse la mafelemu amenewa likhale ndi matabwa awiri ofanana kuyambira pansi mpaka pamwamba. Matabwawo alumikizane pamphete yoyamba. Mafelemu awiriwo apangidwe mofanana ndipo akhale ochirikiza m’makona.
-