Ekisodo 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mafelemuwo uwakute ndi golide,+ ndipo mphete zake zolowetsamo ndodo uzipange ndi golide. Ndodozo uzikute ndi golide.
29 Mafelemuwo uwakute ndi golide,+ ndipo mphete zake zolowetsamo ndodo uzipange ndi golide. Ndodozo uzikute ndi golide.