Ekisodo 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Ukute mafelemuwo ndi golide,+ ndipo mphete zake, zolowetsamo mipiringidzo, uzipange ndi golide. Mipiringidzoyo uikute ndi golide.
29 “Ukute mafelemuwo ndi golide,+ ndipo mphete zake, zolowetsamo mipiringidzo, uzipange ndi golide. Mipiringidzoyo uikute ndi golide.