Ekisodo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa,* mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi kopa.+
3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa,* mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi kopa.+