Ekisodo 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zipilala zonse kuzungulira bwalo lonselo zikhale ndi tolumikizira tasiliva, ndipo tizitsulo tokolowekapo nsalu tikhalenso tasiliva, koma zitsulo zokhazikapo zipilalazo zikhale zakopa.+
17 Zipilala zonse kuzungulira bwalo lonselo zikhale ndi tolumikizira tasiliva, ndipo tizitsulo tokolowekapo nsalu tikhalenso tasiliva, koma zitsulo zokhazikapo zipilalazo zikhale zakopa.+