Ekisodo 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nsanamira zonse kuzungulira bwalo lonselo zikhale ndi mfundo zasiliva, ndipo tizitsulo tokolowekapo nsalu tikhale tasiliva, koma zitsulo zokhazikapo nsanamirazo zikhale zamkuwa.+
17 Nsanamira zonse kuzungulira bwalo lonselo zikhale ndi mfundo zasiliva, ndipo tizitsulo tokolowekapo nsalu tikhale tasiliva, koma zitsulo zokhazikapo nsanamirazo zikhale zamkuwa.+