Ekisodo 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhosayo uiphe nʼkutenga magazi ake ndipo uwawaze mbali zonse za guwa lansembelo.+