Ekisodo 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhosayo uiphe ndi kutenga magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembelo.+