Ekisodo 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako utenge nkhosa ina ija, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa nkhosayo.+