Ekisodo 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Kenako utenge nkhosa inayo, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa nkhosayo.+