Ekisodo 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nyama ya nkhosa yowaikira kuti akhale ansembe ndi mkatewo, zikatsala mpaka mʼmawa, uziwotche ndi moto.+ Siziyenera kudyedwa chifukwa ndi zinthu zopatulika.
34 Nyama ya nkhosa yowaikira kuti akhale ansembe ndi mkatewo, zikatsala mpaka mʼmawa, uziwotche ndi moto.+ Siziyenera kudyedwa chifukwa ndi zinthu zopatulika.