Ekisodo 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nyama ya nkhosa yowalongera unsembe ndi mkatewo, zikatsala mpaka m’mawa mwake, uzitenthe ndi moto.+ Siziyenera kudyedwa chifukwa ndi zinthu zopatulika.
34 Nyama ya nkhosa yowalongera unsembe ndi mkatewo, zikatsala mpaka m’mawa mwake, uzitenthe ndi moto.+ Siziyenera kudyedwa chifukwa ndi zinthu zopatulika.