Ekisodo 29:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndidzaonekera pamenepo kwa Aisiraeli, ndipo malo amenewa adzayeretsedwa ndi ulemerero wanga.+