Ekisodo 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mbali zake zonse 4 zikhale zofanana, mulitali mwake likhale masentimita 45,* mulifupi mwake masentimita 45. Ndipo kutalika kwake kuchoka pansi mpaka pamwamba likhale masentimita 90. Nyanga zake azipangire kumodzi ndi guwalo.*+
2 Mbali zake zonse 4 zikhale zofanana, mulitali mwake likhale masentimita 45,* mulifupi mwake masentimita 45. Ndipo kutalika kwake kuchoka pansi mpaka pamwamba likhale masentimita 90. Nyanga zake azipangire kumodzi ndi guwalo.*+