Ekisodo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Paguwali usaperekerepo zofukiza zosavomerezeka,+ nsembe yopsereza kapena nsembe yambewu, ndipo usathirepo nsembe yachakumwa.
9 Paguwali usaperekerepo zofukiza zosavomerezeka,+ nsembe yopsereza kapena nsembe yambewu, ndipo usathirepo nsembe yachakumwa.