-
Ekisodo 30:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Kenako upere zina mwa zofukiza zimenezi kuti zikhale ufa wosalala kwambiri. Uike wina mwa ufawo patsogolo pa Umboni mʼchihema chokumanako, kumene ndidzaonekera kwa iwe. Zofukiza zimenezi zikhale zopatulika koposa kwa inu.
-