Ekisodo 30:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako upere wina mwa msanganizo umenewu kuti ukhale ufa wosalala kwambiri. Uike wina mwa ufawo patsogolo pa Umboni m’chihema chokumanako,+ kumene ndidzaonekera kwa iwe.+ Msanganizowu ukhale wopatulika koposa kwa inu.
36 Kenako upere wina mwa msanganizo umenewu kuti ukhale ufa wosalala kwambiri. Uike wina mwa ufawo patsogolo pa Umboni m’chihema chokumanako,+ kumene ndidzaonekera kwa iwe.+ Msanganizowu ukhale wopatulika koposa kwa inu.