Ekisodo 30:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Musapange zofukiza zanuzanu pogwiritsa ntchito zinthu zopangira zofukiza zimenezi.+ Muziona kuti zofukiza zimenezi nʼzopatulika kwa Yehova.
37 Musapange zofukiza zanuzanu pogwiritsa ntchito zinthu zopangira zofukiza zimenezi.+ Muziona kuti zofukiza zimenezi nʼzopatulika kwa Yehova.