Ekisodo 30:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Musapange zofukiza zanuzanu pogwiritsa ntchito zinthu zopangira msanganizo umenewu.+ Inu muziona zofukiza zimenezi kukhala zopatulika kwa Yehova.+
37 Musapange zofukiza zanuzanu pogwiritsa ntchito zinthu zopangira msanganizo umenewu.+ Inu muziona zofukiza zimenezi kukhala zopatulika kwa Yehova.+