Ekisodo 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Mose anaitana Bezaleli, Oholiabu ndi mwamuna aliyense waluso amene Yehova anaika nzeru mumtima mwake.+ Anaitana aliyense amene anadzipereka mofunitsitsa kugwira ntchitoyo.+
2 Kenako Mose anaitana Bezaleli, Oholiabu ndi mwamuna aliyense waluso amene Yehova anaika nzeru mumtima mwake.+ Anaitana aliyense amene anadzipereka mofunitsitsa kugwira ntchitoyo.+