-
Ekisodo 37:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kerubi mmodzi anamuika kumbali imodzi ya chivundikirocho ndipo kerubi wina anamuika kumbali inayo. Akerubiwo anawapanga kumapeto onse awiri a chivundikirocho.
-