Ekisodo 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kerubi mmodzi anali kumbali imodzi ya chivundikirocho ndipo kerubi wina kumbali inayo. Akerubiwo anawapanga kumbali zonse ziwiri za chivundikirocho.+
8 Kerubi mmodzi anali kumbali imodzi ya chivundikirocho ndipo kerubi wina kumbali inayo. Akerubiwo anawapanga kumbali zonse ziwiri za chivundikirocho.+