Ekisodo 40:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atatero anayala nsalu+ yophimba pachihemacho ndi inanso yophimba+ pamwamba pake, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
19 Atatero anayala nsalu+ yophimba pachihemacho ndi inanso yophimba+ pamwamba pake, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.