Levitiko 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo aziipha pamaso pa Yehova kumbali yakumpoto ya guwa lansembe. Akatero ana a Aroni ansembe, aziwaza magazi ake mbali zonse za guwa lansembe.+
11 Ndipo aziipha pamaso pa Yehova kumbali yakumpoto ya guwa lansembe. Akatero ana a Aroni ansembe, aziwaza magazi ake mbali zonse za guwa lansembe.+