Levitiko 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nsembe yambewu imene mukupereka kwa Yehova isakhale ndi zofufumitsa,+ chifukwa simukuyenera kuwotcha ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa kapena uchi,* ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 22
11 Nsembe yambewu imene mukupereka kwa Yehova isakhale ndi zofufumitsa,+ chifukwa simukuyenera kuwotcha ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa kapena uchi,* ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.