Levitiko 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nsembe yanu iliyonse yambewu muziithira mchere. Popereka nsembe yambewu musamaiwale kupereka mchere wokukumbutsani pangano la Mulungu. Mukamapereka nsembe iliyonse, muziperekanso mchere.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:13 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 228/15/1999, tsa. 32
13 Nsembe yanu iliyonse yambewu muziithira mchere. Popereka nsembe yambewu musamaiwale kupereka mchere wokukumbutsani pangano la Mulungu. Mukamapereka nsembe iliyonse, muziperekanso mchere.+